Malawi Native Anthem Text Lyrics

National Anthem

1. Mlungu dalitsani Malawi, Mumsunge m'mtendere. Gonjetsani adani onse, Njala, nthenda, nsanje. Lunzitsani mitima yathu, Kuti tisaope. Mdalitse Mtsogo leri na fe, Ndi Mai Malawi. 2. Malawi ndziko lokongola, La chonde ndi ufulu, Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri, Ndithudi tadala. [ From: http://www.metrolyrics.com/malawi-native-anthem-text-lyrics-national-anthem.html ] Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu, N'mphatso zaulere. Nkhalango, madambo abwino. Ngwokoma Malawi. 3. O! Ufulu tigwirizane, Kukweza Malawi. Ndi chikondi, khama, kumvera, Timutumikire. Pa nkhondo nkana pa mtendere, Cholinga n'chimodzi. Mai, bambo, tidzipereke, Pokweza Malawi. Sent by Carlos André Pereira da Silva Branco

Add Tag

Tags

Tell Us What These Lyrics Mean To You...

Mobile Sitehide
Hey, we have a new extension for Chrome: Lyrics for Youtube! More info...